Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino koma osewera ake atsikana ili mdziko la Kenya patsogolo pa masewero awo mawa ndi timu ya dziko-lo.
Lero timuyi ikhala ndi zokonzekera zomaliza.
She Flames squad to Kenya; Amidu, Sikelo, Vinkhumbo, Nyirenda, Madise, Phiri, Jossam, Nyirongo, Vinkhumbo, Ngulube, Mvula, Thom, Dimba, Kapanda, Gondwe, Tabitha,Temwa, Kasenda, Simwaka, Chavinda.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino koma osewera ake atsikana inyamuka mdziko muno kupita ku Kenya komwe akasewere ndi timu ya dziko-lo.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino koma osewera ake atsikana yapambana masewero ake oyamba ndi Kenya pogenjetsa timuyi 3-2.
Minister of Sports, Francis Phiso, has given She Flames team 200,000 Kwacha after a win against Kenya on Wednesday. The money is said to appreciate the hard work shown by the players during the game.