Timu ya Rumphi United yakhala yoyamba kutuluka muligi ya TNM sizoni ino.
Timuyi yapeza mapoint 10 pamasewero 27 amene yasewera muligiyi.
Ngakhale itapambana masewero ake onse atatu, Rumphi United sifikira mapoint a timu yomwe ili pa namba 13 padakali pano yomwe ili ndi mapoint 21.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores