"MPIRA WA CHAKA CHINO SI WAPAKAMWA" - KAMANGA
Mphunzitsi watimu ya Kamuzu Barracks, Charles Kamanga, wati mpira wa chaka chino ndi wovuta kuposa zaka zonse zomwe asewera kamba koti matimu akonzeka kwambiri pa bwalo.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonjetsa Karonga United 2-1 ndipo wati Karonga inasewera bwino kwambiri koma mwayi unali ndi iwo ndipo mpira wapano si wapakamwa.
"Mpira wa chaka chino si wapakamwa chifukwa pa bwalo ukumakakumana ndi zina, kuvutika tikuvutikaku sikuonetsa kuti into ndi ligi yomwe ili yovuta kwaife kuposa a mmbuyomu nde lero Karonga yatikhalitsa kumaka nthawi yonse." Iye anatero.
Timuyi yakwanitsa kupeza zipambano zisanu (5) ndi kufanana mphamvu katatu komanso kugonja kamodzi ndipo ali pa nambala yachiwiri ndi mapointsi 18.
Prediction: 3-1 prediction
Chitipa 1-0 moyale prediction๐ฏ
Prediction 2-1 prediction
Prediction 4-1 prediction
Prediction 1-0 prediction