Gemu inali bwino ngakhale taluza anyamata anali ndi ma chances ambiri kom sanagwiritse km bas ndmene umakhalira mpila ena amawina ena amaluza.