NEWS
Bangwe All Stars yachotsa aphunzitsi awo, Rodgers Yasin komanso Mapopa Msukwa kamba ka kusachita bwino kwa timuyi mu ligi.
Izi ndi malingana ndi zomwe tinalemba sabata yatha kuti timuyi inali pa mkumano ndi aphunzitsiwa ndipo panali kuthekera kuti achoka kutimuyi.
Bangwe ili pa nambala 15 mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 12 pa masewero 19 omwe yasewera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores