NKHANI
Nyuzipepala ya Times yalemba kuti timu ya Silver Strikers ichotsa osewera asanu ndi anayi (9) patsogolo pa ligi yamu chaka cha 2025.
Mdindo wamkulu kutimuyi, Patrick Chimimba, wati osewera angapo awuzidwa kale koma kwatsala awiri omwe akukambirana nawo kuti asiyane mwapaubale mbali zonse zitamvana poti mgwirizano wawo ukadalipo.
Mmodzi mwa osewera yemwe achoke ndi Emmanuel Muyira yemwe mgwirizano wake watha ndi timuyi ndipo ena akhale akulengezedwa zonse zikayenda bwino.
Source: Times
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores