NKHANI
Timu ya Civil Service United yatsimikiza kuti osewera awo atatu, Muhammad Biason, Chikaiko Batson ndi John Dambuleni, awonjezera mgwirizano wawo ndi chaka chimodzi kutimuyi.
Timuyi yatsimikiza nkhaniyi lolemba masana kudzera pa tsamba lawo la mchezo la Facebook.
Pa osewerawa, Batson ndi Biason ndi osewera kutsogolo pomwe Dambuleni amasewera kumbuyo chapakati kutimuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores