Mulibwanji masapota nose a big bulletss, timuyathu yativesa kukoma chaka chino, ndikuyifunila zabwino zose mu top 8, ine JULIO FERNANDO, KU MOCAMBIQUE, OBRIGADO.
Hi
Mulibwanji nose okonda bullets, mulandile ulemu, ine ndikutokoza mulungu pa zimene akutichitira, big mofaya 2022 moto, ana achepa.
Muli bho Maule ๐ฅ๐ฅ