Mmene zayambiratu ndi mmenemo
Mongokumbusana kut ma team akuyenera kut akonzeke bwino coz Ziko Nkanda & Adepoju sanyengerera ma goalkeeper chaka chino
Onse awiri agoletsa lero. Sakunyengereradi chaka chino.
Fixture ndiye yatuluka mpongo ndani pa malawi chaka chino?
A solom perekan fixer mwachangu kaa mwatan
Posachedwapa tikupatsani fixture yonse koma masewero otsugulira ligi ndi a Bullets vs TN Stars pa 13 April ku Kasungu
Kod ku sliver zikut bwanji guss
Bullets ndi Noma amaliza kugula osewera. Bullets yagula Precious Sambani, Luke Chima ndipo Noma yagula Peter Katsonga kungotchula ochepa