Mongokumbusana kut ma team akuyenera kut akonzeke bwino coz Ziko Nkanda & Adepoju sanyengerera ma goalkeeper chaka chino
Mpira ulikodi chaka chino. Achina Stain Davie ndi Khuda Muyaba akonzekeranso.
Onse awiri agoletsa lero. Sakunyengereradi chaka chino.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores