Mphunzitsi wa Silver Strikers, Abbas Makawa, wati achirimika kuti zinthu ziyambireso kuyenda ku timuyi.
Makawa amayankhula izi kutsatira kugonja ndi Civo.
A Makawa ati ndi khumbo lawo kutenga ligi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores