Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
MKONDA WAPITA KU ZAMBIA
Katswiri yemwe wathetsa mgwirizano wake kutimu ya Mighty Mukuru Wanderers, Francis Mkonda, ali mdziko la Zambia komwe akukayesa mwayi kutimu ya Kabwe Warriors ya mdzikomo.
Izi zadziwika malingana ndi mmodzi mwa olemba nkhani mdziko muno, Twaha Chimuka, yemwe wati wapeza kuti osewerayu watuluka kale mdziko muno.
Katswiriyu akhala wachisanu ndi chimodzi ngati anasaine mgwirizano ndi timuyi pa osewera a mdziko muno omwe akusewera mdziko la Zambia komwe kuli Robert Saizi, Chawanangwa Kaonga, Christopher Kumwembe, Emmanuel Savieli ndi Chifundo Mphasi.
Iye anathetsa mgwirizano wake ku Wanderers kamba koti nthawi yosewera imachepa ndipo anati afotokoza bwino za tsogolo lake.
Source: Twaha Silva Chimuka
BREAKING
Francis Mkonda has terminated his contract with Mighty Mukuru Wanderers which was left with 6 months.
The player has confirmed the news through MIJ Online.
The player has struggled to play at the team in the past two seasons and amidst interests from Civil Service United and Creck Sporting Club, the player has ended his stay at Lali Lubani.
Source: MIJ
Francis Mkonda ndi Vincent Nyangulu ayamba kuchita zokonzekera ndi Wanderers pomwe achira.
Awiri-wa ayamba zokonzekera ndi timuyi, Lolemba.
Francis Mkonda has signed a 3 year contract with BE FORWARD Wanderers.
Mkonda is expected to replace Joseph Kamwendo.
Captain wa timu ya Masters Security, Francis Mkonda wawina mphoto ya 2018 Carlsberg Cup Discovery Season Award
Masters Security captain Francis Mkonda has won 2018 Carlsberg Cup Discovery Season award. Mkonda who has been a key player for the club in 2018 season, received 20 votes from 25
FT: EPAC 4 - 1 Kamuzu Barracks (Mphatso Dzongololo, Mude Jeffrey, Anthony Banda, Francis Mkonda - Dan Ziba)