Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
THOM WAPITA KU TP MAZEMBE
Katswiri wa Scorchers, Sabina Thom, atumikira timu ya amayi osewera mpira wamiyendo ya TP Mazembe yaku DRC pomwe wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi.
Katswiriyu anachoka sabata yatha kupita kutimuyi komwe amakayesetsa zachipatala ndipo wakhonza komanso timu yake ya MDF Lionesses yatsimikiza za nkhaniyi. Poyankhula ndi Thom, iye wati ndi okondwa kupita ku timuyi.
"Ndi zokoma kwambiri ndipo ndine osangalala kukhala mbali imodzi ya timu ngati iyiyi ndipo anali maloto anga kutumikira timu yaikulu ngati TP Mazembe." Anafotokozapo Thom.
Katswiriyu wakhala ofunikira kumbali ya Scorchers pomwe anaithandiza kufika mu ndime yotsiriza mu mpikisano wa COSAFA Women's Championship. Iye amasewera pakati chakumanja kapenanso kutsogolo ndipo ndi msilikali wa dziko lino.
Ghana's Thomas Partey who is playing for Arsenal, Thomas Partey likely to miss the opening game in the Premier League.
Partey today sustained an injury in a Mind Charity game against Chelsea.
Get well soon Partey
ThumbsUpPDiv Top Goal Scorers; Brighton Gonani (Neno Medicals) 10 Goals, Humphrey Chimwaza (Sable Farming) and Luis Thom (Sable Farming) have 9 Goals, Ellard Gwetsa and Lanjesi Nkhoma 8 Goals.
Otchinga pa golo wakale wa Dwangwa United, Charles Thom wasaina contract ya zaka zitatu ndi timu ya Silver Strikers.
Katswiri-yu amasewera-nso timu ya Malawi Under 23.
Starting Line Up of Malawi; Charles Thom, Kelvin Kadzinje,Timothy Siliwimba Hadji Wali, Charles Petro, Chinsinsi Maonga, Peter Banda,David Daudi,Auspicious Kadzongola, Andrew Malisero Chikaiko Batison