Phangala yosewera pakati mu timu ya Wanderers, Joseph Kamwendo, wabwera mdziko muno kuchokera kunja komwe amasewera.
Kamwendo anaoneka dzulo pa bwalo la Kamuzu pomwe timu yake, Wanderers, yaluza.
Prediction: 0-1 prediction
Prediction 0-1 prediction
Prediction: 2-1 prediction
Prediction 1-1 prediction