Bungwe la Football Association of Malawi (FAM) lati masewero apakati pa timu ya Civil Sporting ndi Silver Strikers alipo kumathero a sabata ino pa bwalo la Bingu.
Awa ndi masewero amu ndime ya matimu anayi 4, mu mpikisano wa Airtel Top 8.
Timu ya Nyasa Big Bullets inafika kale mu ndime yomaliza ya mpikisano-wu ndipo ikumana ndi opambana pakati pa Civil Sporting ndi Silver Strikers.
CIVO 1- SILVER 3
Prediction 0-2 prediction๐ฏ